Genesis 46:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Awa ndi mayina a ana a Isiraeli, kapena kuti ana a Yakobo, omwe anapita nawo ku Iguputo:+ Mwana woyamba wa Yakobo anali Rubeni.+ 9 Ana a Rubeni anali Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karami.+ Ekisodo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atsogoleri a mafuko a Aisiraeli ndi awa: Ana aamuna a Rubeni, yemwe anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli,+ anali Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karami.+ Amenewa ndi mabanja a fuko la Rubeni.
8 Awa ndi mayina a ana a Isiraeli, kapena kuti ana a Yakobo, omwe anapita nawo ku Iguputo:+ Mwana woyamba wa Yakobo anali Rubeni.+ 9 Ana a Rubeni anali Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karami.+
14 Atsogoleri a mafuko a Aisiraeli ndi awa: Ana aamuna a Rubeni, yemwe anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli,+ anali Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karami.+ Amenewa ndi mabanja a fuko la Rubeni.