Genesis 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, kenako Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni. Genesis 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Simiyoni+ anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli+ mwana wa mkazi wa Chikanani. Ekisodo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana aamuna a Simiyoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli, mwana amene anabereka ndi mkazi wa Chikanani.+ Amenewa ndi mabanja a fuko la Simiyoni. 1 Mbiri 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ana a Simiyoni+ anali Nemueli, Yamini, Yaribi, Zera ndi Shauli.+
23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, kenako Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni.
10 Ana a Simiyoni+ anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli+ mwana wa mkazi wa Chikanani.
15 Ana aamuna a Simiyoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli, mwana amene anabereka ndi mkazi wa Chikanani.+ Amenewa ndi mabanja a fuko la Simiyoni.