Genesis 38:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo mchimwene wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Bwanji ukuchita kungʼamba njira?” Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Perezi.*+ Rute 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mzere wa ana a Perezi+ unayenda chonchi: Perezi anabereka Hezironi,+ Mateyu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yuda anabereka Perezi ndi Zera,+ ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+
29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo mchimwene wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Bwanji ukuchita kungʼamba njira?” Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Perezi.*+
3 Yuda anabereka Perezi ndi Zera,+ ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+