Genesis 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndamuberekera ana aamuna 6.”+ Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+ Genesis 46:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a Zebuloni+ anali Seredi, Eloni ndi Yahaleeli.+
20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndamuberekera ana aamuna 6.”+ Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+