Yoswa 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako fuko la Manase,+ mwana woyamba wa Yosefe,+ linapatsidwa gawo lake.+ Makiri+ mwana woyamba wa Manase, bambo wake wa Giliyadi, anali msilikali wamphamvu, choncho anapatsidwa dera la Giliyadi ndi Basana.+
17 Kenako fuko la Manase,+ mwana woyamba wa Yosefe,+ linapatsidwa gawo lake.+ Makiri+ mwana woyamba wa Manase, bambo wake wa Giliyadi, anali msilikali wamphamvu, choncho anapatsidwa dera la Giliyadi ndi Basana.+