Numeri 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu kwa zaka 40,+ mpaka mʼbadwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+ Numeri 33:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe Aroni anakwera mʼphiri la Hora mogwirizana ndi zimene Yehova analamula, ndipo anamwalira mʼphirimo mʼchaka cha 40 mʼmwezi wa 5 pa tsiku loyamba la mweziwo kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo.+
13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu kwa zaka 40,+ mpaka mʼbadwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+
38 Wansembe Aroni anakwera mʼphiri la Hora mogwirizana ndi zimene Yehova analamula, ndipo anamwalira mʼphirimo mʼchaka cha 40 mʼmwezi wa 5 pa tsiku loyamba la mweziwo kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo.+