Deuteronomo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pajatu Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakusiyani kapena kukuwonongani kapenanso kuiwala pangano limene analumbira kwa makolo anu.+ Yoswa 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe amene adzakugonjetse masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe ngati mmene ndinakhalira ndi Mose+ ndipo sindidzakutaya kapena kukusiya.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+
31 Pajatu Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakusiyani kapena kukuwonongani kapenanso kuiwala pangano limene analumbira kwa makolo anu.+
5 Palibe amene adzakugonjetse masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe ngati mmene ndinakhalira ndi Mose+ ndipo sindidzakutaya kapena kukusiya.+
5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+