Ekisodo 34:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova anapitiriza kuuza Mose kuti: “Ulembe mawuwa+ chifukwa ine ndikuchita pangano ndi iwe komanso Isiraeli mogwirizana ndi mawu amenewa.”+
27 Yehova anapitiriza kuuza Mose kuti: “Ulembe mawuwa+ chifukwa ine ndikuchita pangano ndi iwe komanso Isiraeli mogwirizana ndi mawu amenewa.”+