Ekisodo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova anapitiriza kuuza Mose kuti: “Ndaona kuti anthu amenewa ndi okanika.+ Salimo 78:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akadzachita zimenezi sadzakhala ngati makolo awo,Mʼbadwo wosamva komanso wopanduka,+Mʼbadwo umene mtima wawo unali wosakhazikika*+Komanso wosakhulupirika kwa Mulungu.
8 Akadzachita zimenezi sadzakhala ngati makolo awo,Mʼbadwo wosamva komanso wopanduka,+Mʼbadwo umene mtima wawo unali wosakhazikika*+Komanso wosakhulupirika kwa Mulungu.