Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiyeno mʼtsogolo ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ mudzawayankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi dzanja lake lamphamvu mu Iguputo, mʼnyumba ya ukapolo.+

  • Salimo 44:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,

      Makolo athu anatifotokozera+

      Ntchito zimene inu munachita mu nthawi yawo,

      Mʼmasiku akale.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena