Salimo 96:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+ 1 Akorinto 10:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Sizingatheke kuti muzimwa zamʼkapu ya Yehova* komanso zamʼkapu ya ziwanda. Sizingathekenso kuti muzidya “patebulo la Yehova”*+ komanso patebulo la ziwanda. 22 Kapena ‘kodi tikufuna kuti Yehova* achite nsanje?’+ Kodi mphamvu zathu zingapose mphamvu zake?
5 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+
21 Sizingatheke kuti muzimwa zamʼkapu ya Yehova* komanso zamʼkapu ya ziwanda. Sizingathekenso kuti muzidya “patebulo la Yehova”*+ komanso patebulo la ziwanda. 22 Kapena ‘kodi tikufuna kuti Yehova* achite nsanje?’+ Kodi mphamvu zathu zingapose mphamvu zake?