Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mayiyu ndidzamudzala ngati mbewu zanga padziko lapansi.+

      Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo.*

      Ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Ndinu anthu anga,”*+

      Iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+

  • Aroma 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndi zofanananso ndi zimene ananena mʼbuku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatchula kuti ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sankakondedwa ndidzamutchula kuti ‘wokondedwa.’+

  • Aroma 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno ndifunse kuti, kodi anapunthwa mpaka kugweratu? Ayi. Koma chifukwa cha kulakwa kwawo anthu a mitundu ina apeza chipulumutso, ndipo zimenezi zachititsa kuti olakwawo achite nsanje.+

  • 1 Petulo 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Poyamba simunali anthu a Mulungu, koma tsopano ndinu anthu ake.+ Mulungu anali asanakuchitireni chifundo, koma tsopano wakuchitirani chifundo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena