2 Mbiri 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhale kuti asilikali a Siriya amene anabwera anali ochepa, Yehova anapereka mʼmanja mwawo gulu lalikulu kwambiri la asilikali+ chifukwa iwo anasiya Yehova Mulungu wa makolo awo. Choncho Asiriyawo anapereka chiweruzo kwa Yehoasi.
24 Ngakhale kuti asilikali a Siriya amene anabwera anali ochepa, Yehova anapereka mʼmanja mwawo gulu lalikulu kwambiri la asilikali+ chifukwa iwo anasiya Yehova Mulungu wa makolo awo. Choncho Asiriyawo anapereka chiweruzo kwa Yehoasi.