Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka mʼmanja mwa adani amene anawaukira nʼkutenga zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kulimbana nawo.+ 1 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iwo anaiwala Yehova Mulungu wawo ndipo iye anawapereka*+ kwa Sisera+ mkulu wa asilikali a Hazori, komanso kwa Afilisiti+ ndi kwa mfumu ya Mowabu,+ ndipo onsewa anamenyana nawo.
14 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka mʼmanja mwa adani amene anawaukira nʼkutenga zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kulimbana nawo.+
9 Koma iwo anaiwala Yehova Mulungu wawo ndipo iye anawapereka*+ kwa Sisera+ mkulu wa asilikali a Hazori, komanso kwa Afilisiti+ ndi kwa mfumu ya Mowabu,+ ndipo onsewa anamenyana nawo.