-
Numeri 34:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Malirewo akatsike kuchokera ku Sefamu kulowera ku Ribila, kumʼmawa kwa Aini. Akatsikebe mpaka akadutse pamalo otsetsereka akumʼmawa kwa Nyanja ya Kinereti.*+ 12 Malirewo akatsike ndithu mpaka kumtsinje wa Yorodano, ndipo akathere ku Nyanja Yamchere.+ Limeneli ndi limene lidzakhale dziko lanu+ ndi malire ake olizungulira.’”
-