2 Mafumu 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukaphe anthu a mʼbanja la mbuye wako Ahabu ndipo ine ndidzabwezera magazi a atumiki anga aneneri ndiponso magazi a atumiki onse a Yehova amene Yezebeli anawapha.+ Chivumbulutso 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera mpaka liti, inu Ambuye Wamkulu Koposa, Mulungu woyera ndi woona,+ osaweruza ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi athu?”+
7 Ukaphe anthu a mʼbanja la mbuye wako Ahabu ndipo ine ndidzabwezera magazi a atumiki anga aneneri ndiponso magazi a atumiki onse a Yehova amene Yezebeli anawapha.+
10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera mpaka liti, inu Ambuye Wamkulu Koposa, Mulungu woyera ndi woona,+ osaweruza ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi athu?”+