Ekisodo 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzakumenyerani nkhondo,+ ndipo inu mudzangokhala phee, osachita chilichonse.” Ekisodo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi msilikali wamphamvu.+ Dzina lake ndi Yehova.+ Deuteronomo 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova Mulungu wanu adzakutsogolerani ndipo adzakumenyerani nkhondo,+ ngati mmene anachitira ku Iguputo inu mukuona.+ Deuteronomo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda nanu limodzi kuti akumenyereni nkhondo nʼkukupulumutsani kwa adani anu.’+ Yoswa 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Yoswa anagonjetsa mafumu onsewa nʼkulanda malo awo pa nthawi imodzi, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi amene ankawamenyera nkhondo.+
30 Yehova Mulungu wanu adzakutsogolerani ndipo adzakumenyerani nkhondo,+ ngati mmene anachitira ku Iguputo inu mukuona.+
4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda nanu limodzi kuti akumenyereni nkhondo nʼkukupulumutsani kwa adani anu.’+
42 Yoswa anagonjetsa mafumu onsewa nʼkulanda malo awo pa nthawi imodzi, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi amene ankawamenyera nkhondo.+