Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+ Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+ Deuteronomo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inuyo mukudziwa kuti lero ndikulankhula ndi inu, osati ndi ana anu amene sakudziwa komanso sanaone chilango cha Yehova Mulungu wanu,+ ukulu wake,+ dzanja lake lamphamvu+ komanso mkono wake wotambasula.
16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+ Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+
2 Inuyo mukudziwa kuti lero ndikulankhula ndi inu, osati ndi ana anu amene sakudziwa komanso sanaone chilango cha Yehova Mulungu wanu,+ ukulu wake,+ dzanja lake lamphamvu+ komanso mkono wake wotambasula.