Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pajatu Yehova Mulungu wathu amayankha mapemphero athu nthawi zonse. Kodi pali mtundu winanso wamphamvu umene milungu yake ili nawo pafupi chonchi?+

  • 2 Samueli 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndi mtundu uti padziko lapansi umene ungafanane ndi mtundu wa anthu anu Aisiraeli?+ Inu Mulungu munapita kukawawombola anthu anu+ ndipo munadzipangira dzina+ pamene munawachitira zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha.+ Munathamangitsa mitundu ina ndi milungu yawo chifukwa cha anthu anu amene munawawombola ku Iguputo.

  • Salimo 147:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+

      Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake.

      Tamandani Ya!*+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena