Oweruza 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera apo, mzindawu anaupatsa dzina loti Dani,+ kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani, amene anali mwana wa Isiraeli.+ Koma dzina loyamba la mzindawu linali Laisi.+
29 Kuwonjezera apo, mzindawu anaupatsa dzina loti Dani,+ kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani, amene anali mwana wa Isiraeli.+ Koma dzina loyamba la mzindawu linali Laisi.+