Numeri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine ndipo simunandilemekeze pamaso pa Aisiraeli, simudzalowetsa mpingowu mʼdziko limene ndidzawapatse.”+
12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine ndipo simunandilemekeze pamaso pa Aisiraeli, simudzalowetsa mpingowu mʼdziko limene ndidzawapatse.”+