Ekisodo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova ankalankhula ndi Mose pamasomʼpamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake Yoswa,+ mwana wa Nuni, sankachoka kuchihemako. Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”
11 Yehova ankalankhula ndi Mose pamasomʼpamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake Yoswa,+ mwana wa Nuni, sankachoka kuchihemako.
8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”