Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kwa Aisiraeli amene ankaona zimenezi, ulemerero wa Yehova unkaoneka ngati moto wolilima pamwamba pa phiri.

  • Deuteronomo 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho mudziwe lero kuti Yehova Mulungu wanu awoloka patsogolo panu.+ Iye ndi moto wowononga+ ndipo adzawawononga. Adzawagonjetsa inu mukuona kuti mudzawathamangitse* mwamsanga ndi kuwawononga, mogwirizana ndi zimene Yehova anakulonjezani.+

  • Aheberi 12:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Chifukwa Mulungu wathu ali ngati moto wowononga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena