Ekisodo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lalero limene mwatuluka mu Iguputo,+ mʼnyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova wakutulutsani mʼdzikoli ndi dzanja lake lamphamvu.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi zofufumitsa. Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo, mʼnyumba yaukapolo.+
3 Kenako Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lalero limene mwatuluka mu Iguputo,+ mʼnyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova wakutulutsani mʼdzikoli ndi dzanja lake lamphamvu.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.