Ekisodo 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Dziwani kuti Yehova wakupatsani Sabata.+ Nʼchifukwa chake pa tsiku la 6 akukupatsani chakudya cha masiku awiri. Pa tsiku la 7 aliyense azikhala pamalo ake. Munthu asachoke pamalo ake.”
29 Dziwani kuti Yehova wakupatsani Sabata.+ Nʼchifukwa chake pa tsiku la 6 akukupatsani chakudya cha masiku awiri. Pa tsiku la 7 aliyense azikhala pamalo ake. Munthu asachoke pamalo ake.”