Ekisodo 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzigwira ntchito masiku 6. Koma tsiku la 7 musamagwire ntchito, kuti ngʼombe yanu ndi bulu wanu azipuma, komanso kuti mwana wa kapolo wanu wamkazi ndi mlendo apezenso mphamvu.+
12 Muzigwira ntchito masiku 6. Koma tsiku la 7 musamagwire ntchito, kuti ngʼombe yanu ndi bulu wanu azipuma, komanso kuti mwana wa kapolo wanu wamkazi ndi mlendo apezenso mphamvu.+