-
Deuteronomo 18:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Adzakupatsani mneneriyu poyankha zimene munapempha Yehova Mulungu wanu ku Horebe, tsiku limene munasonkhana kuphiri.+ Paja munapempha kuti, ‘Mutilole kuti tisamvenso mawu a Yehova Mulungu wathu kapena kuona moto waukuluwu, kuopera kuti tingafe.’+ 17 Ndiyeno Yehova anandiuza kuti, ‘Zimene anenazo ndi zabwino.
-