Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+ Salimo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso mtumiki wanu amachenjezedwa nazo.+Munthu wosunga zigamulozo amapeza mphoto yaikulu.+ Yakobo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.
8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+
25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.