Deuteronomo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukagwetse maguwa awo ansembe nʼkuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mukawotche mizati yawo yopatulika* nʼkudula zifaniziro zogoba za milungu yawo,+ ndipo mukachotseretu mayina awo pamalo amenewo.+ 1 Mbiri 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Afilisiti anasiya milungu yawo kumeneko ndipo Davide atalamula, milunguyo anaitentha pamoto.+
3 Mukagwetse maguwa awo ansembe nʼkuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mukawotche mizati yawo yopatulika* nʼkudula zifaniziro zogoba za milungu yawo,+ ndipo mukachotseretu mayina awo pamalo amenewo.+