Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 20:23, 24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kenako Yehova anauza Mose ndi Aroni mʼphiri la Hora, mʼmalire a dziko la Edomu kuti: 24 “Aroni aikidwa mʼmanda ngati mmene zinakhalira ndi makolo ake.*+ Iye sadzalowa mʼdziko limene ndidzapatse Aisiraeli chifukwa awirinu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+

  • Numeri 33:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako ananyamuka ku Mosera nʼkukamanga msasa ku Bene-yaakana.+

  • Numeri 33:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Wansembe Aroni anakwera mʼphiri la Hora mogwirizana ndi zimene Yehova analamula, ndipo anamwalira mʼphirimo mʼchaka cha 40 mʼmwezi wa 5 pa tsiku loyamba la mweziwo kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena