Ekisodo 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mose analowa mumtambomo nʼkukwera mʼphirimo.+ Mose anakhala mmenemo masiku 40, masana ndi usiku.+ Ekisodo 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Mose anakhalabe mʼphirimo ndi Yehova masiku 40, masana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Malamulo Khumi,* pamiyala yosemayo.+
18 Kenako Mose analowa mumtambomo nʼkukwera mʼphirimo.+ Mose anakhala mmenemo masiku 40, masana ndi usiku.+
28 Choncho Mose anakhalabe mʼphirimo ndi Yehova masiku 40, masana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Malamulo Khumi,* pamiyala yosemayo.+