Ekisodo 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musamachitire nkhanza mlendo wokhala pakati panu kapena kumʼpondereza,+ chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+ Levitiko 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mlendo wokhala pakati panu muzimuona ngati mbadwa.+ Muzimukonda ngati mmene mumadzikondera nokha, chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
21 Musamachitire nkhanza mlendo wokhala pakati panu kapena kumʼpondereza,+ chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+
34 Mlendo wokhala pakati panu muzimuona ngati mbadwa.+ Muzimukonda ngati mmene mumadzikondera nokha, chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.