Luka 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira ndipo uyenera kutumikira iye yekha basi.’”+
8 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira ndipo uyenera kutumikira iye yekha basi.’”+