Genesis 46:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Anthu onse amʼnyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+ Ekisodo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana onse a Yakobo komanso zidzukulu zake* analipo 70, koma Yosefe anali kale ku Iguputo.+ Machitidwe 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndiponso abale ake onse.+ Ndipo onse pamodzi analipo anthu 75.+
27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Anthu onse amʼnyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+
14 Choncho Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndiponso abale ake onse.+ Ndipo onse pamodzi analipo anthu 75.+