-
Deuteronomo 17:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ngati pakati panu papezeka mwamuna kapena mkazi amene akuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wanu, mu umodzi mwa mizinda yanu imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani ndipo akuphwanya pangano la Mulungu,+ 3 moti wasochera ndipo amalambira milungu ina nʼkumaigwadira, kapena kugwadira dzuwa, mwezi kapena gulu lonse la zinthu zakuthambo,+ zomwe ine sindinakulamuleni,+
-