-
Deuteronomo 17:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 ndiye munthu wina akakuuzani zimenezi kapena mwamva zimene zachitika, muzifufuza nkhaniyo mosamala. Mukatsimikizira kuti ndi zoonadi+ kuti chinthu choipachi chachitika mu Isiraeli, 5 muzitenga mwamuna kapena mkazi amene wachita chinthu choipayo nʼkupita naye kunja kwa mzinda, ndipo muzikamuponya miyala kuti afe.+
-