Numeri 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Mose anatumiza anthu kuchokera ku Kadesi kupita kwa mfumu ya Edomu+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene takumana nawo. Deuteronomo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musamadane ndi mbadwa ya Edomu, chifukwa ndi mʼbale wanu.+ Musamadane ndi munthu wa ku Iguputo, chifukwa munali alendo mʼdziko lawo.+
14 Kenako Mose anatumiza anthu kuchokera ku Kadesi kupita kwa mfumu ya Edomu+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene takumana nawo.
7 Musamadane ndi mbadwa ya Edomu, chifukwa ndi mʼbale wanu.+ Musamadane ndi munthu wa ku Iguputo, chifukwa munali alendo mʼdziko lawo.+