Ekisodo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawi imeneyo mafumu a ku Edomu adzachita mantha.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera.+ Anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+ Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+
15 Pa nthawi imeneyo mafumu a ku Edomu adzachita mantha.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera.+ Anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+
27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+