Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mʼmalomwake, mudzafunefune Yehova Mulungu wanu pamalo alionse amene adzasankhe kuti aikepo dzina lake komanso malo amene azidzakhala pakati pa mafuko anu onse, ndipo muzidzapita kumeneko.+

  • 1 Mafumu 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako mahule awiri anapita kwa mfumu nʼkuima patsogolo pa mfumuyo.

  • 1 Mafumu 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Aisiraeli onse anamva mmene mfumu inaweruzira nkhaniyo ndipo anachita mantha ndi mfumuyo+ chifukwa anaona kuti Mulungu wamupatsa nzeru kuti aziweruza mwachilungamo.+

  • Salimo 122:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndipo tsopano mapazi athu aima

      Pamageti ako iwe Yerusalemu.+

  • Salimo 122:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Chifukwa kumeneko nʼkumene kunaikidwa mipando yachiweruzo,+

      Mipando yachifumu ya nyumba ya Davide.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena