Deuteronomo 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita zimene Yehova Mulungu wanu wakulamulani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Deuteronomo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Muzionetsetsa kuti mukutsatira mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezerepo kapena kuchotsapo kalikonse.”+
32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita zimene Yehova Mulungu wanu wakulamulani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
32 Muzionetsetsa kuti mukutsatira mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezerepo kapena kuchotsapo kalikonse.”+