Numeri 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula Aisiraeli kuti pacholowa chawo cha malo, akapereke kwa Alevi mizinda yokhalamo.+ Akaperekenso kwa Aleviwo malo odyetserako ziweto ozungulira mizindayo.+
2 “Lamula Aisiraeli kuti pacholowa chawo cha malo, akapereke kwa Alevi mizinda yokhalamo.+ Akaperekenso kwa Aleviwo malo odyetserako ziweto ozungulira mizindayo.+