Levitiko 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Musamadye chilichonse chimene chili ndi magazi.+ Musamaombeze kapena kuchita zamatsenga.+ Machitidwe 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu ambiri amene ankachita zamatsenga anasonkhanitsa mabuku awo nʼkuwatentha pamaso pa anthu onse.+ Ndipo atawerengera mtengo wake anapeza kuti anali okwana ndalama zasiliva zokwana 50,000.
19 Anthu ambiri amene ankachita zamatsenga anasonkhanitsa mabuku awo nʼkuwatentha pamaso pa anthu onse.+ Ndipo atawerengera mtengo wake anapeza kuti anali okwana ndalama zasiliva zokwana 50,000.