Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 26:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chifukwa taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala

      Kuti adzaimbe mlandu anthu okhala mʼdzikoli chifukwa cha zolakwa zawo,

      Ndipo dzikoli lidzaonetsa poyera magazi amene linakhetsa

      Ndipo silidzabisanso anthu ake amene anaphedwa.”

  • Yeremiya 26:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma mudziwe kuti mukandipha, inuyo, mzindawu ndi anthu onse amene akukhala mumzindawu mukhala ndi mlandu wa magazi chifukwa chopha munthu wosalakwa. Ndithudi, Yehova ndi amene wandituma kuti ndidzakuuzeni mawu onse amene mwamvawa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena