Levitiko 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musamaphe ngʼombe kapena nkhosa ndi mwana wake pa tsiku limodzi.+ Salimo 145:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova ndi wabwino kwa aliyense,+Ndipo ntchito zake zonse zimasonyeza kuti ndi wachifundo. Miyambo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama amasamalira ziweto zake,+Koma munthu woipa amaganiza kuti ndi wachifundo, pamene ali wankhanza. Mateyu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mpheta ziwiri amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu,* si choncho? Koma palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+
10 Wolungama amasamalira ziweto zake,+Koma munthu woipa amaganiza kuti ndi wachifundo, pamene ali wankhanza.
29 Mpheta ziwiri amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu,* si choncho? Koma palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+