-
Genesis 34:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Yakobo anamva kuti Sekemu wagwiririra mwana wake Dina. Pa nthawiyo nʼkuti ana ake aamuna ali koweta ziweto zake. Choncho Yakobo sananene kanthu kudikira kuti ana akewo abwere.
-