Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 19:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Choncho ana a Loti awiri onsewo anakhala oyembekezera atagona ndi bambo awo.

  • Genesis 19:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Mwana wamngʼono nayenso anabereka mwana wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Beni-ami. Iye ndi tate wa Aamoni+ amasiku ano.

  • Deuteronomo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno Yehova anandiuza kuti, ‘Usalimbane ndi Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari kwa mbadwa za Loti+ kuti akhale malo awo.

  • Oweruza 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kukanena kuti:

      “Yefita wanena kuti: ‘Aisiraeli sanatenge dziko la Mowabu+ ndi dziko la Aamoni+

  • 2 Mbiri 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano Aamoni, Amowabu ndi anthu akudera lamapiri la Seiri+ abwera. Inu simunalole kuti Aisiraeli alowe mʼdziko lawo pamene ankachokera ku Iguputo ndipo sanawaphe.+

  • Machitidwe 17:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mitundu yonse ya anthu, kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anaika nthawi yoti zinthu zina zizichitika komanso anaika malire a malo oti anthu azikhala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena