Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 19:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Oweruzawo azifufuza nkhaniyo mosamala+ ndipo ngati munthu amene anapereka umboniyo wapezeka kuti amanama ndipo waneneza mʼbale wake mlandu wabodza, 19 muzimuchitira zimene amafuna kuti zichitikire mʼbale wakezo,+ ndipo muzichotsa woipayo pakati panu.+

  • Deuteronomo 21:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 ndipo aziuza akulu amzindawo kuti, ‘Mwana wathuyu ndi wosamva komanso ndi wopanduka ndipo amakana kutimvera. Ndi wosusuka+ komanso ndi chidakwa.’+ 21 Kenako amuna onse a mumzinda wawo azimuponya miyala nʼkumupha. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena