Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:18-20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbadwa* zako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+ 19 Ndidzapereka kwa mbadwa zako dziko la Akeni,+ Akenizi, Akadimoni, 20 Ahiti,+ Aperezi,+ Arefai,+

  • Deuteronomo 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ogi mfumu ya ku Basana ndi amene anali womaliza pa Arefai amene anatsala. Chithatha chimene* anaikapo mtembo wake chinali chachitsulo ndipo mpaka pano chidakali ku Raba wa Aamoni. Mulitali mwake nʼchokwana masentimita 401,* ndipo mulifupi mwake masentimita 178,* potengera muyezo umene unakhazikitsidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena