Genesis 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndi Ahori+ kuphiri lawo la Seiri,+ mpaka kukafika ku Eli-parana, kuchipululu. Deuteronomo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyamba, Ahori+ ankakhala ku Seiri, koma mbadwa za Esau zinawalanda dzikolo nʼkuwapha ndipo iwo anayamba kukhala mʼdzikolo,+ mofanana ndi zimene Aisiraeli adzachite ndi dziko limene ndi cholowa chawo, limene Yehova adzawapatsadi.)
12 Poyamba, Ahori+ ankakhala ku Seiri, koma mbadwa za Esau zinawalanda dzikolo nʼkuwapha ndipo iwo anayamba kukhala mʼdzikolo,+ mofanana ndi zimene Aisiraeli adzachite ndi dziko limene ndi cholowa chawo, limene Yehova adzawapatsadi.)