Genesis 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Isaki anatumiza Yakobo ndipo iye ananyamuka kupita ku Padani-aramu. Anapita kwa Labani mwana wa Betuele, wa Chiaramu.+ Labaniyo anali mchimwene wake wa Rabeka+ amene anali mayi ake a Yakobo ndi Esau. Hoseya 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yakobo anathawira mʼdera la Aramu.*+Ndipo Isiraeli+ ankagwira ntchito kumeneko kuti apeze mkazi,+Ankalondera nkhosa kuti apeze mkazi.+
5 Choncho Isaki anatumiza Yakobo ndipo iye ananyamuka kupita ku Padani-aramu. Anapita kwa Labani mwana wa Betuele, wa Chiaramu.+ Labaniyo anali mchimwene wake wa Rabeka+ amene anali mayi ake a Yakobo ndi Esau.
12 Yakobo anathawira mʼdera la Aramu.*+Ndipo Isiraeli+ ankagwira ntchito kumeneko kuti apeze mkazi,+Ankalondera nkhosa kuti apeze mkazi.+